Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 8:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Benaya+ mwana wa Yehoyada anali mtsogoleri wa Akereti+ ndi Apeleti.+ Ana aamuna a Davide anakhala ansembe.*+

  • 2 Samueli 20:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Yowabu anali mtsogoleri wa gulu lonse lankhondo+ la Isiraeli. Benaya+ mwana wa Yehoyada+ anali kutsogolera Akereti+ ndi Apeleti.+

  • 1 Mafumu 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma wansembe Zadoki,+ Benaya+ mwana wa Yehoyada, mneneri Natani,+ Simeyi,+ Reyi, ndi amuna amphamvu+ a Davide, sanagwirizane+ ndi Adoniya.

  • 1 Mafumu 2:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Kenako Mfumu Solomo inauzidwa kuti: “Yowabu wathawira kuchihema cha Yehova, ndipo ali pambali pa guwa lansembe.” Choncho Solomo anatuma Benaya mwana wa Yehoyada, kuti: “Pita ukamuphe!”+

  • 1 Mbiri 18:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Benaya+ mwana wa Yehoyada+ anali mtsogoleri wa Akereti+ ndi Apeleti,+ ndipo ana aamuna a Davide ndiwo anali ndi udindo waukulu kwambiri pamaso pa mfumu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena