Genesis 31:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yakobo anathawa n’kuwoloka Mtsinje*+ limodzi ndi zonse zimene anali nazo. Atatero, anayenda molunjika dera la kumapiri la Giliyadi.+ Numeri 32:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Choncho Mose anapereka mzinda wa Giliyadi kwa Makiri mwana wa Manase, ndipo iye anayamba kukhala mmenemo.+
21 Yakobo anathawa n’kuwoloka Mtsinje*+ limodzi ndi zonse zimene anali nazo. Atatero, anayenda molunjika dera la kumapiri la Giliyadi.+
40 Choncho Mose anapereka mzinda wa Giliyadi kwa Makiri mwana wa Manase, ndipo iye anayamba kukhala mmenemo.+