1 Mafumu 22:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho Mikaya anati: “Ndikuona Aisiraeli onse atabalalika+ m’mapiri ngati nkhosa zopanda m’busa.+ Ndipo Yehova anati: ‘Amenewa alibe atsogoleri. Aliyense abwerere kunyumba kwake mu mtendere.’”+ Salimo 44:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mwatipereka kwa adani athu kuti atidye ngati nkhosa,+Ndipo mwatimwaza pakati pa anthu a mitundu ina.+ Salimo 95:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti iye ndi Mulungu wathu ndipo ife ndife anthu ake. Iye amatisamalira ngati nkhosa zimene akuweta.+Lero anthu inu mukamvera mawu a Mulungu,+
17 Choncho Mikaya anati: “Ndikuona Aisiraeli onse atabalalika+ m’mapiri ngati nkhosa zopanda m’busa.+ Ndipo Yehova anati: ‘Amenewa alibe atsogoleri. Aliyense abwerere kunyumba kwake mu mtendere.’”+
11 Mwatipereka kwa adani athu kuti atidye ngati nkhosa,+Ndipo mwatimwaza pakati pa anthu a mitundu ina.+
7 Pakuti iye ndi Mulungu wathu ndipo ife ndife anthu ake. Iye amatisamalira ngati nkhosa zimene akuweta.+Lero anthu inu mukamvera mawu a Mulungu,+