Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 16:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Nthawi yomweyo Aroni anatenga chofukiziracho monga anamuuzira Mose, n’kuthamanga kukalowa pakati pa mpingowo. Koma mliri unali utayamba kale pakati pawo. Choncho Aroni anaika nsembe ija pamoto n’kuyamba kuwaphimbira machimo anthuwo.

  • Numeri 25:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Iye anathamangira mwamuna wachiisiraeli uja mpaka kukalowa m’hema wake n’kubaya* awiriwo ndi mkondowo. Anabaya mwamuna wachiisiraeli limodzi ndi mkaziyo, mpaka mkondowo unakadutsa kumaliseche kwa mkaziyo. Pamenepo mliri unaleka pakati pa ana a Isiraeli.+

  • 2 Samueli 24:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pamenepo Yehova anagwetsa mliri+ mu Isiraeli kuyambira m’mawa mpaka nthawi yoikidwiratu, moti pa anthu onse kuyambira ku Dani mpaka ku Beere-seba+ panafa anthu 70,000.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena