Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ngoloyo inafika m’munda wa Yoswa, amene kwawo kunali ku Beti-semesi, ndi kuima pamalo pamene panali mwala waukulu. Ndiyeno anthuwo anawaza matabwa a ngoloyo ndipo ng’ombezo+ anazipereka nsembe yopsereza kwa Yehova.+

  • 1 Mafumu 19:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Choncho anabwerera n’kutenga ng’ombe zamphongo ziwiri n’kuzipha.*+ Anatenga mitengo ya pulawo+ ya ng’ombezo n’kuphikira nyama yake. Kenako anaipereka kwa anthu kuti adye. Atatero, iye ananyamuka n’kutsatira Eliya ndipo anayamba kum’tumikira.+

  • 1 Mbiri 21:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Koma Orinani anauza Davide kuti: “Ingotengani malowa akhale anu,+ ndipo mbuyanga mfumu chitani chilichonse chimene mukuona kuti n’chabwino. Taonani, ineyo ndipereka ng’ombe+ kuti zikhale nsembe zopsereza ndi chopunthira tirigu+ kuti chikhale nkhuni,+ ndiponso ndipereka tirigu kuti akhale nsembe yambewu. Ndikupereka zonsezi.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena