1 Samueli 10:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero Samueli anabweretsa mafuko onse a Isiraeli pafupi,+ ndipo fuko la Benjamini linasankhidwa.+ 1 Samueli 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako anabweretsa pafupi fuko la Benjamini malinga ndi mabanja awo, ndipo banja la Amatiri linasankhidwa.+ Pamapeto pake, Sauli mwana wa Kisi anasankhidwa.+ Choncho anayamba kum’funafuna, koma sanam’peze. 1 Mbiri 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 A fuko la Benjamini,+ abale ake a Sauli,+ analipo 3,000. Kufikira pa nthawiyo, ambiri mwa anthu a fukolo, anali kulondera mosamala nyumba ya Sauli.
20 Chotero Samueli anabweretsa mafuko onse a Isiraeli pafupi,+ ndipo fuko la Benjamini linasankhidwa.+
21 Kenako anabweretsa pafupi fuko la Benjamini malinga ndi mabanja awo, ndipo banja la Amatiri linasankhidwa.+ Pamapeto pake, Sauli mwana wa Kisi anasankhidwa.+ Choncho anayamba kum’funafuna, koma sanam’peze.
29 A fuko la Benjamini,+ abale ake a Sauli,+ analipo 3,000. Kufikira pa nthawiyo, ambiri mwa anthu a fukolo, anali kulondera mosamala nyumba ya Sauli.