Genesis 42:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma iye anawauza kuti: “Mukunama! Mwabwera kuno kudzafufuza malo ofooka a dziko lathu.”+ Genesis 42:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tumani mmodzi pakati panu apite akatenge mng’ono wanuyo. Enanu ndikutsekerani m’ndende. Ndikufuna ndione ngati zimene mukunena zili zoona.+ Ndipo ngati si zoona, pali Farao wamoyo, ndiye kuti ndinu akazitape basi.”
16 Tumani mmodzi pakati panu apite akatenge mng’ono wanuyo. Enanu ndikutsekerani m’ndende. Ndikufuna ndione ngati zimene mukunena zili zoona.+ Ndipo ngati si zoona, pali Farao wamoyo, ndiye kuti ndinu akazitape basi.”