2 Samueli 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Abineri+ mwana wa Nera, amene anali mtsogoleri wa asilikali a Sauli, anatenga Isi-boseti+ mwana wa Sauli ndi kuwolokera naye ku Mahanaimu.+ 2 Samueli 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Tsopano Sauli anali ndi mdzakazi, dzina lake Rizipa,+ mwana wamkazi wa Aya.+ Patapita nthawi, Isi-boseti+ anafunsa Abineri kuti: “N’chifukwa chiyani unagona ndi mdzakazi*+ wa bambo anga?”
8 Ndiyeno Abineri+ mwana wa Nera, amene anali mtsogoleri wa asilikali a Sauli, anatenga Isi-boseti+ mwana wa Sauli ndi kuwolokera naye ku Mahanaimu.+
7 Tsopano Sauli anali ndi mdzakazi, dzina lake Rizipa,+ mwana wamkazi wa Aya.+ Patapita nthawi, Isi-boseti+ anafunsa Abineri kuti: “N’chifukwa chiyani unagona ndi mdzakazi*+ wa bambo anga?”