1 Samueli 20:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno Davide anathawa+ kuchoka ku Nayoti, ku Rama. Koma anapita kwa Yonatani ndi kumuuza kuti: “Kodi ine ndachita chiyani?+ Ndalakwanji, ndipo bambo ako ndawachimwira chiyani kuti azindifunafuna kuti andiphe?” 1 Samueli 20:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Atatero, Sauli anaponya mkondo wake kuti amulase.+ Pamenepo Yonatani anadziwa kuti bambo ake anatsimikiza mtima kupha Davide.+ 1 Samueli 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Davide anapitiriza kukhala mwamantha chifukwa Sauli anali kufunafuna moyo wake, pamene Davideyo anali m’chipululu cha Zifi ku Horesi.*+
20 Ndiyeno Davide anathawa+ kuchoka ku Nayoti, ku Rama. Koma anapita kwa Yonatani ndi kumuuza kuti: “Kodi ine ndachita chiyani?+ Ndalakwanji, ndipo bambo ako ndawachimwira chiyani kuti azindifunafuna kuti andiphe?”
33 Atatero, Sauli anaponya mkondo wake kuti amulase.+ Pamenepo Yonatani anadziwa kuti bambo ake anatsimikiza mtima kupha Davide.+
15 Davide anapitiriza kukhala mwamantha chifukwa Sauli anali kufunafuna moyo wake, pamene Davideyo anali m’chipululu cha Zifi ku Horesi.*+