Genesis 49:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Koma iwe Yuda,+ abale ako adzakutamanda.+ Dzanja lako lidzakhala pambuyo pa khosi la adani ako.+ Ana a bambo ako adzakugwadira.+ 1 Samueli 30:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Davide atafika ku Zikilaga anatumiza zina mwa zofunkhazo kwa mabwenzi ake,+ akulu a ku Yuda, n’kunena kuti: “Landirani mphatso*+ iyi kuchokera pa zimene tafunkha kwa adani a Yehova.”
8 “Koma iwe Yuda,+ abale ako adzakutamanda.+ Dzanja lako lidzakhala pambuyo pa khosi la adani ako.+ Ana a bambo ako adzakugwadira.+
26 Davide atafika ku Zikilaga anatumiza zina mwa zofunkhazo kwa mabwenzi ake,+ akulu a ku Yuda, n’kunena kuti: “Landirani mphatso*+ iyi kuchokera pa zimene tafunkha kwa adani a Yehova.”