Yoswa 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho dzuwa linaimadi, ndiponso mwezi unaima mpaka mtunduwo utalanga adani ake.+ Kodi sizinalembedwe m’buku la Yasari?+ Dzuwa linaima kumwamba pakatikati, silinafulumire kulowa pafupifupi kwa tsiku lonse lathunthu.+
13 Choncho dzuwa linaimadi, ndiponso mwezi unaima mpaka mtunduwo utalanga adani ake.+ Kodi sizinalembedwe m’buku la Yasari?+ Dzuwa linaima kumwamba pakatikati, silinafulumire kulowa pafupifupi kwa tsiku lonse lathunthu.+