1 Mbiri 17:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Tsopano inu Yehova, ndinu Mulungu woona,+ ndipo mwandilonjeza ine mtumiki wanu zabwino zimenezi.+