1 Mbiri 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako, Nahasi+ mfumu ya ana a Amoni anamwalira, ndipo mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwa bambo akewo.+
19 Kenako, Nahasi+ mfumu ya ana a Amoni anamwalira, ndipo mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwa bambo akewo.+