Yoswa 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atatero, anatentha ndi moto mzindawo ndi zonse zimene zinali mmenemo.+ Koma siliva, golide, zipangizo zamkuwa ndi zachitsulo, anazipereka kuti zipite ku chuma cha nyumba ya Yehova.+ Yoswa 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mizinda ya fuko la ana a Benjamini potsata mabanja awo inali Yeriko,+ Beti-hogila, Emeki-kezizi, 1 Mbiri 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pambuyo pake anthu anauza Davide zimene zinachitikira atumiki ake aja, ndipo iye nthawi yomweyo anatumiza mthenga kuti akakumane nawo chifukwa atumikiwo anachititsidwa manyazi kwambiri. Choncho mfumu inawauza kuti: “Mukhalebe ku Yeriko+ kufikira ndevu zanu zitakula ndithu, kenako mudzabwere.”
24 Atatero, anatentha ndi moto mzindawo ndi zonse zimene zinali mmenemo.+ Koma siliva, golide, zipangizo zamkuwa ndi zachitsulo, anazipereka kuti zipite ku chuma cha nyumba ya Yehova.+
5 Pambuyo pake anthu anauza Davide zimene zinachitikira atumiki ake aja, ndipo iye nthawi yomweyo anatumiza mthenga kuti akakumane nawo chifukwa atumikiwo anachititsidwa manyazi kwambiri. Choncho mfumu inawauza kuti: “Mukhalebe ku Yeriko+ kufikira ndevu zanu zitakula ndithu, kenako mudzabwere.”