1 Samueli 31:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno tsiku lotsatira, Afilisiti atabwera kudzavula zovala anthu ophedwa,+ anapeza Sauli ndi ana ake atatu atafa paphiri la Giliboa.+ 2 Samueli 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Isiraeli iwe, anthu ako aulemerero aphedwa pamalo ako okwezeka.+Haa! Anthu amphamvu agwa.
8 Ndiyeno tsiku lotsatira, Afilisiti atabwera kudzavula zovala anthu ophedwa,+ anapeza Sauli ndi ana ake atatu atafa paphiri la Giliboa.+