1 Samueli 25:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Nthawi yomweyo, ananyamuka ndi kugwada mpaka nkhope yake pansi,+ n’kunena kuti: “Ine kapolo wanu ndine wokonzeka kukhala mtumiki wosambitsa mapazi+ a atumiki a mbuyanga.”+
41 Nthawi yomweyo, ananyamuka ndi kugwada mpaka nkhope yake pansi,+ n’kunena kuti: “Ine kapolo wanu ndine wokonzeka kukhala mtumiki wosambitsa mapazi+ a atumiki a mbuyanga.”+