Salimo 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komanso mundiletse kuchita modzikuza, ine mtumiki wanu.+Musalole kuti kudzikuza kundilamulire.+Pamenepo ndidzakhala wopanda chifukwa,+Ndipo ndidzakhalabe wopanda milandu yambiri yophwanya malamulo.
13 Komanso mundiletse kuchita modzikuza, ine mtumiki wanu.+Musalole kuti kudzikuza kundilamulire.+Pamenepo ndidzakhala wopanda chifukwa,+Ndipo ndidzakhalabe wopanda milandu yambiri yophwanya malamulo.