2 Samueli 11:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Davide anatuma nthumwi kuti akamutenge.+ Choncho mkaziyo anabweradi kwa Davide+ ndipo Davide anagona naye+ pa nthawi imene mkaziyo anali kudziyeretsa ku chodetsa chake.+ Zitatero mkaziyo anabwerera kunyumba yake.
4 Kenako Davide anatuma nthumwi kuti akamutenge.+ Choncho mkaziyo anabweradi kwa Davide+ ndipo Davide anagona naye+ pa nthawi imene mkaziyo anali kudziyeretsa ku chodetsa chake.+ Zitatero mkaziyo anabwerera kunyumba yake.