1 Samueli 25:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Patapita masiku 10, Yehova anakantha+ Nabala ndipo anafa. 2 Samueli 24:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo Yehova anagwetsa mliri+ mu Isiraeli kuyambira m’mawa mpaka nthawi yoikidwiratu, moti pa anthu onse kuyambira ku Dani mpaka ku Beere-seba+ panafa anthu 70,000.+
15 Pamenepo Yehova anagwetsa mliri+ mu Isiraeli kuyambira m’mawa mpaka nthawi yoikidwiratu, moti pa anthu onse kuyambira ku Dani mpaka ku Beere-seba+ panafa anthu 70,000.+