2 Samueli 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno mkazi wina wanzeru+ mumzindawo anayamba kufuula kuti: “Tamverani amuna inu, tamverani! Chonde muuzeni Yowabu kuti abwere pafupipa kuti ndilankhule naye.”
16 Ndiyeno mkazi wina wanzeru+ mumzindawo anayamba kufuula kuti: “Tamverani amuna inu, tamverani! Chonde muuzeni Yowabu kuti abwere pafupipa kuti ndilankhule naye.”