Genesis 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Zitatero, Kaini anauza Abele m’bale wake kuti: “Tiye tipite kumunda.” Ali kumeneko, Kaini anam’kantha Abele m’bale wake n’kumupha.+ Ekisodo 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma tsiku lotsatira atapitanso, anapeza amuna awiri achiheberi akumenyana. Choncho anafunsa wolakwayo kuti: “Ukum’menyeranji mnzako?”+
8 Zitatero, Kaini anauza Abele m’bale wake kuti: “Tiye tipite kumunda.” Ali kumeneko, Kaini anam’kantha Abele m’bale wake n’kumupha.+
13 Koma tsiku lotsatira atapitanso, anapeza amuna awiri achiheberi akumenyana. Choncho anafunsa wolakwayo kuti: “Ukum’menyeranji mnzako?”+