Genesis 4:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Lero ndiye mukundipitikitsa pamalo ano ndi pamaso panu.+ Ndidzakhala woyendayenda+ ndi wothawathawa padziko lapansi, ndipo n’zoonekeratu kuti aliyense wondipeza, adzandipha ndithu.”+
14 Lero ndiye mukundipitikitsa pamalo ano ndi pamaso panu.+ Ndidzakhala woyendayenda+ ndi wothawathawa padziko lapansi, ndipo n’zoonekeratu kuti aliyense wondipeza, adzandipha ndithu.”+