Numeri 35:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Wobwezera magazi+ ndi amene ayenera kupha wakupha munthuyo. Akadzangom’peza, wobwezera magaziyo adzamuphe. Deuteronomo 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 akulu a mumzinda wakwawo azitumiza anthu kukam’tenga kumeneko, ndipo azim’pereka m’manja mwa wobwezera magazi kuti afe ndithu.+
19 “‘Wobwezera magazi+ ndi amene ayenera kupha wakupha munthuyo. Akadzangom’peza, wobwezera magaziyo adzamuphe.
12 akulu a mumzinda wakwawo azitumiza anthu kukam’tenga kumeneko, ndipo azim’pereka m’manja mwa wobwezera magazi kuti afe ndithu.+