Genesis 27:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mayi ake anamuyankha kuti: “Temberero limenelo libwere kwa ine m’malo mwa iwe mwana wanga.+ Ingomvera zimene ndanenazi. Pita ukanditengere ana a mbuziwo.”+ 1 Samueli 25:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako anagwada pamapazi+ a Davide ndi kunena kuti: “Zolakwa zonse zikhale pa ine+ mbuyanga. Chonde, lolani kapolo wanu wamkazi alankhule nanu+ ndipo mvetserani mawu a kapolo wanu.
13 Koma mayi ake anamuyankha kuti: “Temberero limenelo libwere kwa ine m’malo mwa iwe mwana wanga.+ Ingomvera zimene ndanenazi. Pita ukanditengere ana a mbuziwo.”+
24 Kenako anagwada pamapazi+ a Davide ndi kunena kuti: “Zolakwa zonse zikhale pa ine+ mbuyanga. Chonde, lolani kapolo wanu wamkazi alankhule nanu+ ndipo mvetserani mawu a kapolo wanu.