Ekisodo 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho Farao anauza Mose kuti: “Choka!+ Samala! Ndisadzakuonenso, chifukwa ndikadzangokuonanso udzafa.”+ 2 Samueli 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Davide anamuyankha kuti: “Chabwino! Ineyo ndichitadi nawe pangano. Koma ndikukupempha chinthu chimodzi ichi, ‘Usadzaone nkhope yanga+ pokhapokha utabweretsa Mikala,+ mwana wamkazi wa Sauli pobwera kuno.’”
28 Choncho Farao anauza Mose kuti: “Choka!+ Samala! Ndisadzakuonenso, chifukwa ndikadzangokuonanso udzafa.”+
13 Davide anamuyankha kuti: “Chabwino! Ineyo ndichitadi nawe pangano. Koma ndikukupempha chinthu chimodzi ichi, ‘Usadzaone nkhope yanga+ pokhapokha utabweretsa Mikala,+ mwana wamkazi wa Sauli pobwera kuno.’”