Numeri 32:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Tsopano ana a Rubeni+ ndi ana a Gadi+ anakhala ndi ziweto zambiri, zankhaninkhani. Iwo anayamba kusirira dziko la Yazeri+ ndi la Giliyadi, ndipo deralo linalidi malo abwino a ziweto. Yoswa 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anapatsidwanso dera la Giliyadi, la Agesuri,+ la Amaakati, phiri lonse la Herimoni,+ ndi dera lonse la Basana+ mpaka ku Saleka.+
32 Tsopano ana a Rubeni+ ndi ana a Gadi+ anakhala ndi ziweto zambiri, zankhaninkhani. Iwo anayamba kusirira dziko la Yazeri+ ndi la Giliyadi, ndipo deralo linalidi malo abwino a ziweto.
11 Anapatsidwanso dera la Giliyadi, la Agesuri,+ la Amaakati, phiri lonse la Herimoni,+ ndi dera lonse la Basana+ mpaka ku Saleka.+