2 Samueli 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano lupanga+ silidzachoka panyumba yako mpaka kalekale.+ Chimenechi n’chotsatira cha zimene unachita chifukwa chondinyoza mwa kutenga mkazi wa Uriya Mhiti kukhala mkazi wako.’
10 Tsopano lupanga+ silidzachoka panyumba yako mpaka kalekale.+ Chimenechi n’chotsatira cha zimene unachita chifukwa chondinyoza mwa kutenga mkazi wa Uriya Mhiti kukhala mkazi wako.’