2 Samueli 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako Simeyi+ mwana wa Gera,+ wa fuko la Benjamini, wochokera ku Bahurimu,+ pamodzi ndi amuna a ku Yuda anapita mofulumira kukakumana ndi Mfumu Davide.
16 Kenako Simeyi+ mwana wa Gera,+ wa fuko la Benjamini, wochokera ku Bahurimu,+ pamodzi ndi amuna a ku Yuda anapita mofulumira kukakumana ndi Mfumu Davide.