Mateyu 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mwachitsanzo, Mulungu ananena kuti, ‘Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako.’+ Komanso anati, ‘Aliyense wonenera bambo ake kapena mayi ake zachipongwe afe ndithu.’+ 2 Timoteyo 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 osakonda achibale awo,+ osafuna kugwirizana ndi anzawo,+ onenera anzawo zoipa,+ osadziletsa, oopsa,+ osakonda zabwino,+
4 Mwachitsanzo, Mulungu ananena kuti, ‘Uzilemekeza bambo ako ndi mayi ako.’+ Komanso anati, ‘Aliyense wonenera bambo ake kapena mayi ake zachipongwe afe ndithu.’+
3 osakonda achibale awo,+ osafuna kugwirizana ndi anzawo,+ onenera anzawo zoipa,+ osadziletsa, oopsa,+ osakonda zabwino,+