2 Samueli 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndiyeno pamene Davide anafika pamwamba pa phiri pamene anthu anali kugwadira Mulungu, anaona Husai+ Mwareki+ akubwera kudzakumana naye, atang’amba chovala chake ndiponso atadzithira dothi kumutu.+ 2 Samueli 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno Husai+ Mwareki,+ mnzake wa Davide,+ atangofika kwa Abisalomu anauza Abisalomu kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!+ Mfumu ikhale ndi moyo wautali!”
32 Ndiyeno pamene Davide anafika pamwamba pa phiri pamene anthu anali kugwadira Mulungu, anaona Husai+ Mwareki+ akubwera kudzakumana naye, atang’amba chovala chake ndiponso atadzithira dothi kumutu.+
16 Ndiyeno Husai+ Mwareki,+ mnzake wa Davide,+ atangofika kwa Abisalomu anauza Abisalomu kuti: “Mfumu ikhale ndi moyo wautali!+ Mfumu ikhale ndi moyo wautali!”