22Choncho Davide anachoka kumeneko+ ndi kuthawira+ kuphanga+ la Adulamu.+ Abale ake ndi nyumba yonse ya bambo ake anamva zimenezo, ndipo ananyamuka kumutsatira.
19 Kenako amuna a ku Zifi+ anapita kwa Sauli ku Gibeya+ kukamuuza kuti: “Kodi Davide si uyu akubisala+ pafupi ndi ife m’malo ovuta kufikamo ku Horesi,+ paphiri la Hakila+ limene lili kudzanja lamanja* la Yesimoni?*+