2 Samueli 17:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndimupeza ali wotopa ndi wofooka manja ake onse,+ ndipo adzanjenjemera ndithu chifukwa cha ine. Pamenepo anthu onse amene ali naye adzathawa, ndipo ine ndidzapha mfumu ili yokha.+
2 Ndimupeza ali wotopa ndi wofooka manja ake onse,+ ndipo adzanjenjemera ndithu chifukwa cha ine. Pamenepo anthu onse amene ali naye adzathawa, ndipo ine ndidzapha mfumu ili yokha.+