Miyambo 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Munthu amene sadziwa zinthu amakhulupirira mawu alionse,+ koma wochenjera amaganizira za mmene akuyendera.+ Miyambo 25:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ulemerero wa Mulungu ndiwo kusunga chinsinsi,+ ndipo ulemerero wa mafumu ndiwo kufufuza bwino nkhani.+
15 Munthu amene sadziwa zinthu amakhulupirira mawu alionse,+ koma wochenjera amaganizira za mmene akuyendera.+
2 Ulemerero wa Mulungu ndiwo kusunga chinsinsi,+ ndipo ulemerero wa mafumu ndiwo kufufuza bwino nkhani.+