1 Samueli 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Idzaika anthu ena kukhala atsogoleri a magulu a anthu 1,000+ ndi atsogoleri a magulu a anthu 50.+ Ena azidzalima minda yake+ ndi kukolola mbewu zake,+ ndiponso ena azidzapanga zida zake zankhondo+ ndi zida zogwiritsa ntchito pamagaleta ake.+ 1 Mbiri 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano Davide anakambirana ndi mkulu aliyense wa anthu 1,000, wa anthu 100 ndiponso mtsogoleri aliyense.+ 1 Akorinto 14:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Koma zinthu zonse zizichitika moyenera ndi mwadongosolo.+
12 Idzaika anthu ena kukhala atsogoleri a magulu a anthu 1,000+ ndi atsogoleri a magulu a anthu 50.+ Ena azidzalima minda yake+ ndi kukolola mbewu zake,+ ndiponso ena azidzapanga zida zake zankhondo+ ndi zida zogwiritsa ntchito pamagaleta ake.+
13 Tsopano Davide anakambirana ndi mkulu aliyense wa anthu 1,000, wa anthu 100 ndiponso mtsogoleri aliyense.+