Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pa tsiku limenelo, kumenyana kunakula ndipo kunali koopsa kwambiri. Pamapeto pake, Abineri+ ndi amuna a Isiraeli anagonjetsedwa ndi atumiki a Davide.

  • 2 Mbiri 13:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kenako ana a Isiraeli anayamba kuthawa pamaso pa Ayuda, koma Mulungu anawapereka m’manja mwa Ayudawo.+

  • 2 Mbiri 28:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Chotero Peka+ mwana wa Remaliya+ anakapha anthu 120,000 ku Yuda tsiku limodzi. Onse amene anaphedwawo anali amuna olimba mtima. Iwo anaphedwa chifukwa chakuti anasiya Yehova+ Mulungu wa makolo awo.

  • Salimo 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Nyamukani,+ inu Yehova! Ndipulumutseni+ inu Mulungu wanga!+

      Pakuti mudzakantha adani anga onse pachibwano.+

      Mano a anthu oipa mudzawaphwanyaphwanya.+

  • Miyambo 24:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 pakuti tsoka lawo lidzagwa mwadzidzidzi,+ ndipo ndani angadziwe za kufafanizika kwa anthu ofuna kuti zinthu zisinthe?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena