Miyambo 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mkwiyo wa mfumu umatanthauza amithenga a imfa,+ koma munthu wanzeru ndi amene amauziziritsa.+ Miyambo 24:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mwana wanga uziopa Yehova ndiponso mfumu.+ Usamakhale pagulu la anthu ofuna kuti zinthu zisinthe,+
21 Mwana wanga uziopa Yehova ndiponso mfumu.+ Usamakhale pagulu la anthu ofuna kuti zinthu zisinthe,+