Numeri 27:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi dzina la bambo athu lichotsedwe ku banja lawo chifukwa chakuti analibe mwana wamwamuna?+ Chonde, tipatseni cholowa pakati pa abale awo a bambo athu.”+ 2 Samueli 14:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Abisalomu anabereka ana aamuna atatu+ ndi mwana wamkazi mmodzi, dzina lake Tamara. Ameneyu anali chiphadzuwa chadzaoneni.+
4 Kodi dzina la bambo athu lichotsedwe ku banja lawo chifukwa chakuti analibe mwana wamwamuna?+ Chonde, tipatseni cholowa pakati pa abale awo a bambo athu.”+
27 Abisalomu anabereka ana aamuna atatu+ ndi mwana wamkazi mmodzi, dzina lake Tamara. Ameneyu anali chiphadzuwa chadzaoneni.+