2 Samueli 15:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Taona, iwo ali ndi ana amuna awiri, Ahimazi+ mwana wa Zadoki ndi Yonatani+ mwana wa Abiyatara. Choncho amuna inu mukatume amenewa kuti adzandiuze zonse zimene mungamve.” 2 Samueli 17:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamene Yonatani+ ndi Ahimazi+ anali ataimirira pa Eni-rogeli,+ kapolo wamkazi anapita kumeneko ndi kuwauza zonse. Choncho iwo anachoka pakuti anafunika kukauza Mfumu Davide. Iwowa sanayese n’komwe kulowa mumzinda kuopera kuti angawazindikire.
36 Taona, iwo ali ndi ana amuna awiri, Ahimazi+ mwana wa Zadoki ndi Yonatani+ mwana wa Abiyatara. Choncho amuna inu mukatume amenewa kuti adzandiuze zonse zimene mungamve.”
17 Pamene Yonatani+ ndi Ahimazi+ anali ataimirira pa Eni-rogeli,+ kapolo wamkazi anapita kumeneko ndi kuwauza zonse. Choncho iwo anachoka pakuti anafunika kukauza Mfumu Davide. Iwowa sanayese n’komwe kulowa mumzinda kuopera kuti angawazindikire.