Genesis 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ana a Hamu anali Kusi,+ Miziraimu,+ Puti+ ndi Kanani.+ Numeri 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano Miriamu ndi Aroni anayamba kum’nena Mose chifukwa cha mkazi wachikusi amene anam’kwatira.+ 2 Mbiri 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pambuyo pake Zera Mwitiyopiya+ anabwera kudzamenyana nawo ali ndi gulu lankhondo la asilikali 1,000,000+ ndi magaleta 300, ndipo anafika ku Maresha.+
12 Tsopano Miriamu ndi Aroni anayamba kum’nena Mose chifukwa cha mkazi wachikusi amene anam’kwatira.+
9 Pambuyo pake Zera Mwitiyopiya+ anabwera kudzamenyana nawo ali ndi gulu lankhondo la asilikali 1,000,000+ ndi magaleta 300, ndipo anafika ku Maresha.+