1 Samueli 26:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano Abisai anauza Davide kuti: “Lero Mulungu wapereka mdani wako m’manja mwako.+ Ndiye ndilole chonde, ndimubaye ndi kumukhomerera pansi ndi mkondo kamodzi kokha, sindichita kubwereza kawiri.” Salimo 31:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Simunandipereke m’manja mwa adani.+Mwapondetsa phazi langa pamalo otakasuka.+
8 Tsopano Abisai anauza Davide kuti: “Lero Mulungu wapereka mdani wako m’manja mwako.+ Ndiye ndilole chonde, ndimubaye ndi kumukhomerera pansi ndi mkondo kamodzi kokha, sindichita kubwereza kawiri.”