Oweruza 5:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Inu Yehova, adani anu onse afafanizidwe chimodzimodzi,+Ndipo okukondani inu+ akhale amphamvu ngati mmene dzuwa limakhalira.”+Choncho, dzikolo linakhala pa mtendere zaka 40.+ Salimo 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu ochita zoipa atandiyandikira kuti adye mnofu wanga,+Popeza kuti iwo ndi ondiukira komanso adani anga,+Anapunthwa ndi kugwa.+ Salimo 68:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Mulungu anyamuke,+ adani ake amwazike,+Ndipo amene amadana naye kwambiri athawe pamaso pake.+
31 Inu Yehova, adani anu onse afafanizidwe chimodzimodzi,+Ndipo okukondani inu+ akhale amphamvu ngati mmene dzuwa limakhalira.”+Choncho, dzikolo linakhala pa mtendere zaka 40.+
2 Anthu ochita zoipa atandiyandikira kuti adye mnofu wanga,+Popeza kuti iwo ndi ondiukira komanso adani anga,+Anapunthwa ndi kugwa.+