2 Samueli 17:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Davide anafika ku Mahanaimu+ ndipo Abisalomu nayenso anawoloka Yorodano pamodzi ndi amuna onse a Isiraeli amene anali naye. 2 Samueli 19:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Barizilai anali wokalamba kwambiri pakuti anali ndi zaka 80.+ Pamene mfumu inali kukhala ku Mahanaimu,+ Barizilai anali kuipatsa chakudya pakuti iye anali munthu wolemera kwambiri.+
24 Davide anafika ku Mahanaimu+ ndipo Abisalomu nayenso anawoloka Yorodano pamodzi ndi amuna onse a Isiraeli amene anali naye.
32 Barizilai anali wokalamba kwambiri pakuti anali ndi zaka 80.+ Pamene mfumu inali kukhala ku Mahanaimu,+ Barizilai anali kuipatsa chakudya pakuti iye anali munthu wolemera kwambiri.+