2 Samueli 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pambuyo pa zinthu zimenezi, zinachitika kuti, Abisalomu+ mwana wa Davide, anali ndi mlongo wake wokongola dzina lake Tamara.+ Ndipo Aminoni+ mwana wa Davide anayamba kukonda kwambiri+ Tamara.
13 Pambuyo pa zinthu zimenezi, zinachitika kuti, Abisalomu+ mwana wa Davide, anali ndi mlongo wake wokongola dzina lake Tamara.+ Ndipo Aminoni+ mwana wa Davide anayamba kukonda kwambiri+ Tamara.