Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 25:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Tsopano mbuyanga, ndikulumbira pali Yehova, Mulungu wamoyo,+ komanso pali moyo wanu:+ Yehova wakubwezani+ kuti musapalamule mlandu wamagazi+ komanso kuti musadzipulumutse nokha ndi dzanja lanu.+ Choncho lolani kuti adani anu ndi onse ofuna kukuvulazani mbuyanga, akhale ngati Nabala.+

  • 1 Mafumu 2:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Tsopano m’dzina la Yehova Mulungu wamoyo,+ amene wandichititsa kukhazikika,+ amene wandiika pampando wachifumu wa Davide bambo anga,+ ndiponso amene anandipatsa mzere wa banja lachifumu+ monga ananenera,+ lero Adoniya aphedwa.”+

  • 2 Mafumu 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Kenako Eliya anauza Elisa kuti: “Iweyo khala apa, pakuti ine Yehova wandituma ku Beteli.” Koma Elisa anati: “Pali Yehova Mulungu wamoyo+ ndiponso pali moyo wanu,+ sindikusiyani.”+ Choncho iwo anapita ku Beteli.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena