2 Samueli 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pamapeto pake anatenga Abisalomu ndi kum’ponya m’dzenje lalikulu m’nkhalangomo ndipo anamuunjikira mulu waukulu kwambiri wa miyala.+ Koma Aisiraeli onse, aliyense anathawira kunyumba yake. 1 Mafumu 22:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kenako, dzuwa litatsala pang’ono kulowa, mumsasamo munamveka mfuu yaikulu, yakuti: “Aliyense azipita kumzinda wake, ndi kudziko lake!”+
17 Pamapeto pake anatenga Abisalomu ndi kum’ponya m’dzenje lalikulu m’nkhalangomo ndipo anamuunjikira mulu waukulu kwambiri wa miyala.+ Koma Aisiraeli onse, aliyense anathawira kunyumba yake.
36 Kenako, dzuwa litatsala pang’ono kulowa, mumsasamo munamveka mfuu yaikulu, yakuti: “Aliyense azipita kumzinda wake, ndi kudziko lake!”+