Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 17:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Choncho Davide, mwa kugwiritsa ntchito gulaye ndi mwala, anali wamphamvu kuposa Mfilisiti. Iye anamukantha ndi kumupha, ndipo m’manja mwa Davide munalibe lupanga.+

  • 1 Samueli 18:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Akazi amene anali kusangalalawo anali kuimba molandizana mawu kuti:

      “Sauli wakantha adani ake masauzande,

      Ndipo Davide wakantha masauzande makumimakumi.”+

  • 1 Samueli 19:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Iye anaika moyo wake pangozi*+ n’kupha Mfilisiti uja,+ moti Yehova anapereka chipulumutso chachikulu+ kwa Aisiraeli onse. Inuyo munaona zimenezi zikuchitika, ndipo munasangalala. Ndiye n’chifukwa chiyani mukufuna kuchimwira magazi osalakwa, mwa kupha Davide+ popanda chifukwa?”+

  • 2 Samueli 5:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pamenepo Davide anachitadi momwemo, monga mmene Yehova anamulamulira,+ moti anapha+ Afilisiti kuchokera ku Geba*+ mpaka kukafika ku Gezeri.+

  • 2 Samueli 8:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pamene Asiriya a ku Damasiko+ anabwera kudzathandiza Hadadezeri mfumu ya Zoba, Davide anapha amuna 22,000 a ku Siriya.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena