Oweruza 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Chonde lankhulani nzika zonse za Sekemu zikumva, kuti, ‘Chabwino n’chiti kwa inu, kuti amuna 70,+ ana onse a Yerubaala akulamulireni, kapena munthu mmodzi akulamulireni? Ndipotu kumbukirani kuti ine ndine fupa lanu ndi mnofu wanu.’”+ 2 Samueli 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Patapita nthawi, mafuko onse a Isiraeli anapita kwa Davide+ ku Heburoni+ ndi kumuuza kuti: “Ife ndife fupa lanu ndi mnofu wanu.+
2 “Chonde lankhulani nzika zonse za Sekemu zikumva, kuti, ‘Chabwino n’chiti kwa inu, kuti amuna 70,+ ana onse a Yerubaala akulamulireni, kapena munthu mmodzi akulamulireni? Ndipotu kumbukirani kuti ine ndine fupa lanu ndi mnofu wanu.’”+
5 Patapita nthawi, mafuko onse a Isiraeli anapita kwa Davide+ ku Heburoni+ ndi kumuuza kuti: “Ife ndife fupa lanu ndi mnofu wanu.+