1 Samueli 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Poyankha Sauli anati: “Ndachimwa.+ Bwerera mwana wanga Davide, pakuti sindidzakuvulaza chifukwa moyo wanga wakhala wamtengo wapatali+ kwa iwe lero. Taona, ndachita zinthu mopusa ndipo ndalakwitsa kwambiri.” 2 Samueli 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Mfumu Davide inafika ku Bahurimu.+ Kumeneko inaona mwamuna wina wa m’banja la Sauli, dzina lake Simeyi,+ mwana wa Gera akutuluka ndipo anali kulankhula mawu onyoza.+
21 Poyankha Sauli anati: “Ndachimwa.+ Bwerera mwana wanga Davide, pakuti sindidzakuvulaza chifukwa moyo wanga wakhala wamtengo wapatali+ kwa iwe lero. Taona, ndachita zinthu mopusa ndipo ndalakwitsa kwambiri.”
5 Ndiyeno Mfumu Davide inafika ku Bahurimu.+ Kumeneko inaona mwamuna wina wa m’banja la Sauli, dzina lake Simeyi,+ mwana wa Gera akutuluka ndipo anali kulankhula mawu onyoza.+