-
2 Samueli 13:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Zitatero, m’bale wake Abisalomu+ anamuuza kuti: “Kodi si m’bale wako Aminoni+ amene wakuchitira choipa chimenechi? Tsopano khala chete mlongo wanga. Iyeyo ndi m’bale wako.+ Usadandaule ndi nkhani imeneyi.” Ndiyeno Tamara anayamba kukhala kunyumba ya m’bale wake Abisalomu ndipo sanali kucheza ndi wina aliyense.
-
-
2 Samueli 13:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Tsopano mbuyanga mfumu, musavutike mtima ndi mawu amenewa onena kuti, ‘Ana onse a mfumu afa,’ pakuti ndi Aminoni yekha amene wafa.”
-