Mlaliki 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwana wosauka koma wanzeru ali bwino+ kuposa mfumu yokalamba koma yopusa,+ imene sionanso kufunika kochenjezedwa.+ Maliko 10:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Sizili choncho pakati panu. Koma aliyense wofuna kukhala wamkulu pakati panu ayenera kukhala mtumiki wanu.+
13 Mwana wosauka koma wanzeru ali bwino+ kuposa mfumu yokalamba koma yopusa,+ imene sionanso kufunika kochenjezedwa.+
43 Sizili choncho pakati panu. Koma aliyense wofuna kukhala wamkulu pakati panu ayenera kukhala mtumiki wanu.+